1 Samueli 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Davide anafunsiranso kwa Yehova.+ Ndipo Yehova anamuyankha kuti: “Nyamuka, pita ku Keila, chifukwa ndipereka Afilisitiwo mʼmanja mwako.”+
4 Choncho Davide anafunsiranso kwa Yehova.+ Ndipo Yehova anamuyankha kuti: “Nyamuka, pita ku Keila, chifukwa ndipereka Afilisitiwo mʼmanja mwako.”+