-
1 Samueli 23:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno Davide anafunsanso kuti: “Kodi atsogoleri amumzinda wa Keila adzandipereka kwa Sauli pamodzi ndi amuna amene ndili nawowa?” Yehova anayankha kuti: “Inde adzakupereka.”
-