1 Samueli 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yomweyo Davide ananyamuka pamodzi ndi amuna pafupifupi 600 amene anali naye aja.+ Iwo anachoka ku Keila nʼkumapita kulikonse kumene angakhale otetezeka. Sauli atamva kuti Davide wathawa ku Keila, sanamutsatirenso.
13 Nthawi yomweyo Davide ananyamuka pamodzi ndi amuna pafupifupi 600 amene anali naye aja.+ Iwo anachoka ku Keila nʼkumapita kulikonse kumene angakhale otetezeka. Sauli atamva kuti Davide wathawa ku Keila, sanamutsatirenso.