1 Samueli 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno anamuuza kuti: “Usachite mantha, chifukwa Sauli bambo anga sakupeza, moti iwe ukhaladi mfumu ya Isiraeli,+ ndipo ine ndidzakhala wachiwiri kwa iwe. Sauli bambo anga akudziwa bwino zimenezi.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:17 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,12/1/1993, tsa. 24
17 Ndiyeno anamuuza kuti: “Usachite mantha, chifukwa Sauli bambo anga sakupeza, moti iwe ukhaladi mfumu ya Isiraeli,+ ndipo ine ndidzakhala wachiwiri kwa iwe. Sauli bambo anga akudziwa bwino zimenezi.”+