-
1 Samueli 23:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndiye ndikupempha kuti mukafufuze malo enieni amene akukhala komanso munthu amene anamuona, chifukwa ndamva kuti ndi wochenjera kwambiri.
-