1 Samueli 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho iwo anamusiya Sauli nʼkutsogola kupita ku Zifi.+ Apa nʼkuti Davide ndi amuna amene ankayenda naye ali mʼchipululu cha Maoni,+ ku Araba,+ kumʼmwera kwa Yesimoni.
24 Choncho iwo anamusiya Sauli nʼkutsogola kupita ku Zifi.+ Apa nʼkuti Davide ndi amuna amene ankayenda naye ali mʼchipululu cha Maoni,+ ku Araba,+ kumʼmwera kwa Yesimoni.