1 Samueli 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho ndi mawu amenewa, Davide analetsa* anthu amene anali naye kuti asachitire Sauli choipa chilichonse. Kenako Sauli anatuluka mʼphangamo nʼkumapita.
7 Choncho ndi mawu amenewa, Davide analetsa* anthu amene anali naye kuti asachitire Sauli choipa chilichonse. Kenako Sauli anatuluka mʼphangamo nʼkumapita.