1 Samueli 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi yomweyo, Abigayeli+ anatenga mikate 200, mitsuko iwiri ikuluikulu ya vinyo komanso anapha nkhosa 5. Anatenganso tirigu wokazinga wokwana miyezo 5 ya seya,* makeke 100 a mphesa zouma ndiponso makeke 200 a nkhuyu zouma nʼkuzikweza pa abulu.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:18 Tsanzirani, ptsa. 79-80 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 20
18 Nthawi yomweyo, Abigayeli+ anatenga mikate 200, mitsuko iwiri ikuluikulu ya vinyo komanso anapha nkhosa 5. Anatenganso tirigu wokazinga wokwana miyezo 5 ya seya,* makeke 100 a mphesa zouma ndiponso makeke 200 a nkhuyu zouma nʼkuzikweza pa abulu.+