-
1 Samueli 25:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Abigayeli ataona Davide, nthawi yomweyo anatsika pabulu wake ndipo anagwada patsogolo pa Davide nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi.
-