1 Samueli 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Sauli ananyamuka nʼkupita kuchipululu cha Zifi ndi amuna 3,000 osankhidwa mu Isiraeli kuti akafunefune Davide kuchipululuko.+
2 Choncho Sauli ananyamuka nʼkupita kuchipululu cha Zifi ndi amuna 3,000 osankhidwa mu Isiraeli kuti akafunefune Davide kuchipululuko.+