-
1 Samueli 26:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho Davide ndi Abisai anapita kwa asilikaliwo usiku. Atafika anaona Sauli atagona pakati pa msasawo, mkondo wake atauzika pansi chakumutu kwake. Ndipo Abineri ndi asilikali ena onse anali atagona momuzungulira.
-