1 Samueli 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndikaiganizira nkhaniyi mmene Yehova akuionera, sindingayerekeze kuvulaza wodzozedwa wa Yehova.+ Ingotenga mkondo umene uli chakumutu kwakewo ndi jagi ya dothi ya madziyo tizipita.”
11 Ndikaiganizira nkhaniyi mmene Yehova akuionera, sindingayerekeze kuvulaza wodzozedwa wa Yehova.+ Ingotenga mkondo umene uli chakumutu kwakewo ndi jagi ya dothi ya madziyo tizipita.”