-
1 Samueli 26:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako Davide anapita kutsidya lina nʼkukaima pamwamba pa phiri, chapatali. Pakati pawo panali kamtunda ndithu.
-