1 Samueli 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Davide anauza Abineri kuti: “Kodi si iwe mwamuna? Ndani angafanane nawe mu Isiraeli? Ndiye nʼchifukwa chiyani walephera kuyangʼanira mbuye wako mfumu? Msilikali winatu anabwera kumeneko kuti adzaphe mbuye wako mfumu!+
15 Ndiyeno Davide anauza Abineri kuti: “Kodi si iwe mwamuna? Ndani angafanane nawe mu Isiraeli? Ndiye nʼchifukwa chiyani walephera kuyangʼanira mbuye wako mfumu? Msilikali winatu anabwera kumeneko kuti adzaphe mbuye wako mfumu!+