1 Samueli 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ine lero ndaona moyo wanu kukhala wamtengo wapatali. Mofanana ndi zimenezi, moyo wanganso ukhale wamtengo wapatali pamaso pa Yehova ndipo andipulumutse mʼmasautso anga onse.”+
24 Ine lero ndaona moyo wanu kukhala wamtengo wapatali. Mofanana ndi zimenezi, moyo wanganso ukhale wamtengo wapatali pamaso pa Yehova ndipo andipulumutse mʼmasautso anga onse.”+