-
1 Samueli 27:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Davide anauza Akisi kuti: “Ngati mungandikomere mtima, ndimapempha kuti andipatseko malo mumzinda umodzi wakutali kuti ndikakhale kumeneko. Palibe chifukwa choti ine mtumiki wanu ndizikhala limodzi ndi inu mumzinda wachifumu.”
-