1 Samueli 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Davide akapita kunkhondo sankasiya mwamuna kapena mkazi aliyense wamoyo.+ Iye ankatenga nkhosa, ngʼombe, abulu, ngamila ndi zovala ndipo akatero ankabwerera kwa Akisi.
9 Davide akapita kunkhondo sankasiya mwamuna kapena mkazi aliyense wamoyo.+ Iye ankatenga nkhosa, ngʼombe, abulu, ngamila ndi zovala ndipo akatero ankabwerera kwa Akisi.