-
1 Samueli 27:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Davide sankasiya mwamuna kapena mkazi aliyense wamoyo nʼkubwerera naye ku Gati, chifukwa ankaganiza kuti: “Angayambe kukatinenera kuti, ‘Davide wachita zakutizakuti.’” (Izi nʼzimene iye ankachita pa nthawi yonse imene anakhala mumzinda wakutali wa Afilisiti.)
-