1 Samueli 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sauli ankafunsira kwa Yehova+ koma Yehova sankamuyankha, kaya kudzera mʼmaloto, Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.
6 Sauli ankafunsira kwa Yehova+ koma Yehova sankamuyankha, kaya kudzera mʼmaloto, Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.