1 Samueli 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mkaziyo anauza Sauli kuti: “Iwe ukudziwa zimene Sauli anachita. Paja anachotsa mʼdzikoli anthu olankhula ndi mizimu ndiponso olosera zamʼtsogolo.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani ukufuna kunditchera msampha kuti ndiphedwe?”+
9 Koma mkaziyo anauza Sauli kuti: “Iwe ukudziwa zimene Sauli anachita. Paja anachotsa mʼdzikoli anthu olankhula ndi mizimu ndiponso olosera zamʼtsogolo.+ Ndiye nʼchifukwa chiyani ukufuna kunditchera msampha kuti ndiphedwe?”+