1 Samueli 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Achita zimenezi chifukwa sunamvere mawu a Yehova, ndipo sunasonyeze mkwiyo wake pamene anakwiyira kwambiri Aamaleki.+ Nʼchifukwa chaketu Yehova akukuchitira zimenezi lero.
18 Achita zimenezi chifukwa sunamvere mawu a Yehova, ndipo sunasonyeze mkwiyo wake pamene anakwiyira kwambiri Aamaleki.+ Nʼchifukwa chaketu Yehova akukuchitira zimenezi lero.