-
1 Samueli 28:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Nthawi yomweyo, Sauli anagwa ndipo anagona pansi kwalaa, chifukwa anachita mantha kwambiri ndi zimene “Samueli” ananena. Komanso analefuka kwambiri chifukwa sanadye masana onse ndi usiku wonse.
-