-
1 Samueli 28:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndiye chonde ndimvereni ine mtumiki wanu. Ndikufuna ndikupatseni mkate kuti mudye nʼcholinga choti mupezenso mphamvu pa ulendo wanu.”
-