-
1 Samueli 28:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma iye anakana ndipo anati: “Sindidya.” Koma atumiki ake ndi mzimayiyo anamukakamiza kuti adye. Kenako anawamvera ndipo anadzuka pamene anagonapo nʼkukakhala pabedi.
-