-
1 Samueli 29:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma Davide anayankha Akisi kuti: “Ndibwerere chifukwa chiyani? Ndakulakwirani chiyani ine mtumiki wanu, kuyambira tsiku limene ndinabwera kudzakhala nanu mpaka lero? Ndisapite kukamenyana ndi adani anu mbuyanga mfumu chifukwa chiyani?”
-