1 Samueli 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aamalekiwo anatenga akazi+ amumzindawo komanso anthu ena onse, kuyambira mwana mpaka wamkulu. Sanaphe aliyense koma anangowatenga nʼkumapita nawo.
2 Aamalekiwo anatenga akazi+ amumzindawo komanso anthu ena onse, kuyambira mwana mpaka wamkulu. Sanaphe aliyense koma anangowatenga nʼkumapita nawo.