1 Samueli 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akazi awiri a Davide nawonso anatengedwa, Ahinowamu wa ku Yezereeli ndi Abigayeli amene anali mkazi wa Nabala wa ku Karimeli.+
5 Akazi awiri a Davide nawonso anatengedwa, Ahinowamu wa ku Yezereeli ndi Abigayeli amene anali mkazi wa Nabala wa ku Karimeli.+