-
1 Samueli 30:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiyeno anapeza munthu wina wa ku Iguputo patchire. Anamutenga nʼkupita naye kwa Davide ndipo anamupatsa chakudya ndi madzi akumwa.
-