-
1 Samueli 30:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Ndiwe kapolo wa ndani, nanga kwanu nʼkuti?” Munthuyo anayankha kuti: “Ndine wa ku Iguputo, kapolo wa Mwamaleki, koma mbuyanga anandisiya pano masiku atatu apitawa nditayamba kudwala.
-