1 Samueli 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Palibe chinthu chawo chilichonse chimene chinasowa, ngakhale chachingʼono. Anapulumutsa ana awo aamuna ndi aakazi komanso zonse zimene anatenga.+ Davide anapulumutsa zonse zimene iwo anatenga.
19 Palibe chinthu chawo chilichonse chimene chinasowa, ngakhale chachingʼono. Anapulumutsa ana awo aamuna ndi aakazi komanso zonse zimene anatenga.+ Davide anapulumutsa zonse zimene iwo anatenga.