1 Samueli 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Davide anati: “Ayi abale anga, musatero ndi zinthu zimene Yehova watipatsa. Iye watiteteza ndiponso wapereka mʼmanja mwathu gulu la achifwamba limene linadzatiukira.+
23 Koma Davide anati: “Ayi abale anga, musatero ndi zinthu zimene Yehova watipatsa. Iye watiteteza ndiponso wapereka mʼmanja mwathu gulu la achifwamba limene linadzatiukira.+