-
1 Samueli 31:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 asilikali onse ananyamuka nʼkuyenda usiku wonse ndipo anakachotsa mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake pakhoma la mzinda wa Beti-sani. Kenako anabwerera ku Yabesi nʼkutentha mitemboyo kumeneko.
-