-
2 Samueli 1:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno Davide anafunsa mnyamata amene anabweretsa uthengawo kuti: “Kodi kwanu nʼkuti?” Iye anayankha kuti: “Ndine mwana wa Mwamaleki, amene anabwera kudzakhala ndi Aisiraeli.”
-