2 Samueli 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu mapiri a Giliboa,+Mame kapena mvula zisagwe pa inu.Komanso minda yakumeneko isatulutse zopereka zopatulika.+Chifukwa chishango cha amuna amphamvu chinadetsedwa kumeneko,Chishango cha Sauli sichikupakidwanso mafuta.
21 Inu mapiri a Giliboa,+Mame kapena mvula zisagwe pa inu.Komanso minda yakumeneko isatulutse zopereka zopatulika.+Chifukwa chishango cha amuna amphamvu chinadetsedwa kumeneko,Chishango cha Sauli sichikupakidwanso mafuta.