2 Samueli 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sauli ndi Yonatani+ anali okondedwa ndi osangalatsa pa moyo wawo,Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+ Anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+Amphamvu kuposa mikango.+
23 Sauli ndi Yonatani+ anali okondedwa ndi osangalatsa pa moyo wawo,Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+ Anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+Amphamvu kuposa mikango.+