2 Samueli 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Isiraeli iwe, anthu amphamvu agwa pankhondo! Yonatani waphedwa pamalo ako okwezeka!+