-
2 Samueli 2:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho iwo ananyamuka. Kumbali ya Benjamini ndi Isi-boseti, mwana wa Sauli, anasankha anyamata 12 ndipo kwa atumiki a Davide anasankhanso anyamata 12.
-