-
2 Samueli 2:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mnyamata aliyense anagwira mnzake kumutu ndipo aliyense anabaya mnzake ndi lupanga mʼmimba moti onsewo anafa. Malo amenewo, omwe ali ku Gibiyoni, anawapatsa dzina lakuti Helikati-hazurimu.
-