-
2 Samueli 2:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako Abineri anamuuza kuti: “Khotera kumanja kapena kumanzere ugwire mmodzi mwa anyamatawo ndipo utenge zimene ungamuvule.” Koma Asaheli anapitirizabe kumuthamangitsa.
-