-
2 Samueli 2:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Yowabu anayankha kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Mulungu woona, ukanapanda kulankhula, anthuwa akanapitiriza kuthamangitsa abale awo mpaka mʼmawa.”
-