2 Samueli 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Abineri ndi anthu ake anayenda kudutsa ku Araba+ usiku wonse mpaka anakawoloka Yorodano. Iwo anayenda kudutsa chigwa* chonse mpaka kukafika ku Mahanaimu.+
29 Abineri ndi anthu ake anayenda kudutsa ku Araba+ usiku wonse mpaka anakawoloka Yorodano. Iwo anayenda kudutsa chigwa* chonse mpaka kukafika ku Mahanaimu.+