-
2 Samueli 2:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Yowabu atasiya kuthamangitsa Abineri anasonkhanitsa anthu onse. Pagulu la atumiki a Davide panasowa Asaheli ndi amuna ena 19.
-