2 Samueli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iwo ananyamula mtembo wa Asaheli+ nʼkukauika mʼmanda a bambo ake ku Betelehemu.+ Kenako Yowabu ndi amuna amene anali naye anayenda usiku wonse ndipo anafika ku Heburoni+ kukucha.
32 Iwo ananyamula mtembo wa Asaheli+ nʼkukauika mʼmanda a bambo ake ku Betelehemu.+ Kenako Yowabu ndi amuna amene anali naye anayenda usiku wonse ndipo anafika ku Heburoni+ kukucha.