2 Samueli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene nkhondo ya pakati pa anthu a nyumba ya Sauli ndi a nyumba ya Davide inkapitirira, Abineri+ anaonetsetsa kuti akupitiriza kukhala ndi mphamvu mʼnyumba ya Sauli.
6 Pamene nkhondo ya pakati pa anthu a nyumba ya Sauli ndi a nyumba ya Davide inkapitirira, Abineri+ anaonetsetsa kuti akupitiriza kukhala ndi mphamvu mʼnyumba ya Sauli.