2 Samueli 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi yomweyo, Abineri anatumiza anthu kwa Davide kukamuuza kuti: “Kodi dzikoli ndi la ndani?” Anawonjezera kuti: “Chitani nane pangano, ndipo ineyo ndidzayesetsa kuti Aisiraeli onse akhale kumbali yanu.”+
12 Nthawi yomweyo, Abineri anatumiza anthu kwa Davide kukamuuza kuti: “Kodi dzikoli ndi la ndani?” Anawonjezera kuti: “Chitani nane pangano, ndipo ineyo ndidzayesetsa kuti Aisiraeli onse akhale kumbali yanu.”+