2 Samueli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiye dziwani zochita chifukwa Yehova anauza Davide kuti:+ ‘Ndidzapulumutsa anthu anga Aisiraeli kwa Afilisiti ndiponso kwa adani awo onse pogwiritsa ntchito dzanja la Davide mtumiki wanga.’”
18 Ndiye dziwani zochita chifukwa Yehova anauza Davide kuti:+ ‘Ndidzapulumutsa anthu anga Aisiraeli kwa Afilisiti ndiponso kwa adani awo onse pogwiritsa ntchito dzanja la Davide mtumiki wanga.’”