2 Samueli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Abineri analankhula ndi anthu a fuko la Benjamini.+ Anapitanso kukalankhula ndi Davide pa awiri ku Heburoni ndipo anamuuza zimene Aisiraeli komanso anthu onse a nyumba ya Benjamini anagwirizana.
19 Kenako Abineri analankhula ndi anthu a fuko la Benjamini.+ Anapitanso kukalankhula ndi Davide pa awiri ku Heburoni ndipo anamuuza zimene Aisiraeli komanso anthu onse a nyumba ya Benjamini anagwirizana.