-
2 Samueli 3:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kenako Abineri anauza Davide kuti: “Ine ndimati ndinyamuke ndikasonkhanitse Aisiraeli onse kuti akhale mbali ya mbuyanga mfumu, kuti achite nanu pangano ndipo mudzakhala mfumu ya anthu onse amene mumafuna kuwalamulira.” Choncho Davide analola Abineri kuti apite mwamtendere.
-