2 Samueli 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yowabu+ atafika pamodzi ndi gulu lonse lankhondo lomwe anali nalo, anthu anamuuza kuti: “Abineri+ mwana wa Nera+ anabwera kwa mfumu, ndipo mfumu yamulola kupita mwamtendere.”
23 Yowabu+ atafika pamodzi ndi gulu lonse lankhondo lomwe anali nalo, anthu anamuuza kuti: “Abineri+ mwana wa Nera+ anabwera kwa mfumu, ndipo mfumu yamulola kupita mwamtendere.”