-
2 Samueli 3:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Zitatero Yowabu anapita kwa mfumu nʼkunena kuti: “Nʼchiyani mwachitachi? Abineri anabwera kwa inu. Ndiye zoona mungamusiye kuti azipita mwamtendere?
-